Khristu Mu Nyimbo

No description added.

Chichewa 220 Songs

Mmamawa Kapena Poturuka Dzuwa

[1]
Mmamawa kapena poturuka dzuwa, Ambuye Yesuyo ’dzafika mphamvu
Ndi ulemerero wokuru kutenga Anthu ace mu ace mu dzikoli.

Chorus:
Yesu, Mbuye wathu, ’Dzayimba mokondwa liti?
Kristu adza, Kristu adza, Aleluya amen, Aleluya amen.

[2]
Kapena usana kapena madzulo, Kapena usiku pamene Ambuye
’Dzafika mu ulemerero kutenga Anthu ace mu dzikoli.

[3]
Tidzakondwa ngati tidzanka osafa, Opanda kudwala, cisoni maliro;
Kungokhwathulidwa podzadza kutenga anthu ace mu dzikoli.

[4]
Tidzakondwa ngati tidzanka osafa, Opanda kudwala, cisoni, maliro;
Kungokhwathulidwa podzadzza kutenga Anthu ace mu dzikoli.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffee Buy us a coffee

Like this song


Share this song

Lyrics Videos on Youtube

A wonderful Saviour A wonderful Saviour Spiritual Songs
WHAT A FRIEND WE HAVE IN JESUS WHAT A FRIEND WE HAVE IN JESUS Songs Of Prayer And Praise
Glory Glory Songs On Request
DOES JESUS CARE? DOES JESUS CARE? Hymns Of Comfort
Jesus My Savior Jesus My Savior Songs On Request
Kutembea Nawe Kutembea Nawe Kiswahili Praise And Worship