Khristu Mu Nyimbo

No description added.

Chichewa 220 Songs

Mlungu Watisunga ’Fe

[1]
Mlungu watisunga ’fe Mpaka mlungu winawu;
T’yeni timpembedze ’Ye, Tsiku lopumali;
Tiganize zinthu za Mau a Mlunguyo.
Tiganize zinthu za Mau a Mulunguyo.

[2]
Pakufuna nsisizo, Zakudzera m’dzinalo,
Mudze, Mbuye wathu ’Nu, Mukhululukire ’fe;
Pakupuma mwanumo, Tikumbuka Inuyo.
Pakupuma mwanumo, Tikumbuka inuyo.

[3]
Pakulemekeza ’Nu, Tikuyandikira ’Nu;
Tikuona mphamvuyo, Ndi ulemererowo.
Mtithangate Mbuyathu Kudya phwando m’mwamba
Mtithangate Mbuyathu kudya pwando m’mwamba

[4]
Mbuye mugonjetsetu Chimo la mu mtimanga,
Kuti ndikagwiretu Ntchito zokondwetsa ’Nu.
Masabata onsewo Alingane momwemo,
Masabata onsewo Alingane momwemo.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffee Buy us a coffee

Like this song


Share this song

Lyrics Videos on Youtube

AMAZING GRACE AMAZING GRACE Hymns Of Comfort
Wings Of A Dove Wings Of A Dove Golden Bells
Does Jesus Care Does Jesus Care Golden Bells
He Gave Me A Song He Gave Me A Song Songs On Request
Wade In The Water Wade In The Water Songs On Request
Joy To The World Joy To The World Caroling Songs