Loading Songs...

Mlendo Ali Pa Khomo

[1]
Mlendo ali pa khomo, Mlowetse (Mlowetsenitu, Mlowetsenitu).
Wadza kale kalelo, Mlowetse (Mlowetsenitu, Mlowetsenitu).
Mtsegulire msangatu, Wakuyerayerayo,
Mwana wa Mulunguyo, Mlowetse (Mlowetsenitu, Mlowetsenitu).

[2]
Utsegule mtimawo, Mlowetse (Mlowetsenitu, Mlowetsenitu).
Ukacedwa ’cokatu, Mloewtse (Mlowetsenitu, Mlowetsenitu).
Ndiye bwenzi lakolo, ’Dzakupulumutsa ’we;
’Dzakusamaliranso, Mlowetse (Mlowetsenitu, Mlowetsenitu).

[3]
Imva mau acewo, Mlowetse (MLowetsenitu, Mlowetsenitu),
Sanka iye leroli, Mlowetsenetu, (Mlowetsenitu, Mlowetsenitu),
Wangoima khomopo, ’Dzakusangalatsa ’we,
Udzamlemekezatu, Mlowetse (Mlowetsenitu, Mlowetsenitu).

[4]
Mlendo wa kumwambayo, Mlowetse (Mlowetsenitu, MLowetsenitu),
’Dzakupatsa zonsezo, Mlowetse (Mlowetsenitu, Mlowetsenitu).
’Dzakhululukira ’we, Ndipo potsirizapo
’Dzakutenga mmwambamo, Mlowetse (Mlowetsenitu, Mlowetsenitu).



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

1 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

What A Friend We Have In Jesus What A Friend We Have In Jesus
Christ In Song Hymnal
Hide Me, Rock Of Ages Hide Me, Rock Of Ages
Songs On Request
Mungu Mkuu Mungu Mkuu
Kiswahili Praise And Worship
Amazing Grace Amazing Grace
Spiritual Songs
ABIDE WITH ME ABIDE WITH ME
Hymns Of Comfort