Khristu Mu Nyimbo

No description added.

Chichewa 220 Songs

Maziko Amodzi

[1]
Maziko a mpingo amodzi ndi Kristu;
Colenga catsopano, mwa madzi ndi mau;
Anatsika kumwamba nalenga mpingowo;
Naugula ndi mwazi naufera mpingo.

[2]
Wokwanira mitundu yonse ya pa dziko;
Koma cipulumutso mwa njira imodzi,
Dzinali loyeretsa lapanga mpingowu,
Cogaawira cimodzi cisomo coyera.

[3]
Ponyoza mpingo wace anthu adzaona,
Adani apasula Thanthwe sadzalitha;
Oyerawo osunga cikhulupiriro;
Cisoni cikadzatha, tidzakondwerera.

[4]
M’kati mwa masauko a mpingo woyera;
Mpingo ulindirira cipulumutsoco;
Maso otopa nako kulira kukwera;
Mpingo waukuruwo udzagonjetsadi.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffee Buy us a coffee

Like this song


Share this song

Lyrics Videos on Youtube

Holy, Holy, Holy Holy, Holy, Holy Hillsong United
AMAZING GRACE AMAZING GRACE Hymns Of Comfort
Ancient Words Ancient Words Golden Bells
Blessed Assurance Blessed Assurance Christ In Song Hymnal