Masika A Dziko Ayandika
[1]
Masika a dziko ayandikatu, Aitana Mbuye okololawo;
Ndi mina yeyera pa dziko lonse, Ndi mwini zotuta wayandikanso.
Chorus:
’Dzanitu msanga, Tengatu zotuta; Mdzatitengae ’fe, Kwathuko
Alto, Tenor, ndi Bass;
Idzanitu angelo, msangatu; Tengereni zotuta mmwambamo.
Mudzatengetu ife, kunkatu, Kwathu mmwambamo.
[2]
E, tsiku lopanda misozi konse, Layandika kudza mothamangatu;
Akubalalika ndi ucimowo, Mwasonkhetu nthawi isanathei.
[3]
Ikomatu ntchito ya cikondico, Kasupe wosaphwa wa kumwambako;
Cikonditu ndico ciitana ’fe, Cigwiritsa ntchito, Cibalitsatu.
Support Mysongbooks
Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.
Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.