Loading Songs...

M’manja A Yesu Wanga

[1]
M’manja a Yesu wanga ndiri kugonamo,
Mommo aphimba ine naco cikondico.
Mvera! Mudzera mmwamba mau a Yesu wanga,
Mwana ndisungira pano pa matima panga

Chorus:
M’manja a Yesu wanga ndiri kugonamo,
Mommo aphimmba ine naco cikondico.

[2]
M’manja a Yesu wanga nkhawa zonsezi zi!
Momwe zoipa zanga sizindibvuta bi.
Mommo mulibe nsoni, mommo mokoma monse.
Sindiliramo msozi, nkondwa ndi Mtima wonse.

[3]
Mtima umabisala m’manja mwa Yesumo,
Mbuye musunge ine, ndikhulupira ’Nu.
Mommo wa cete ine mpaka wocoka mdima,
Tsono ndiona komwe Yesu wokoma Mtima.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

0 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

10000 Reasons 10000 Reasons
Songs On Request
BLESSED ASSURANCE BLESSED ASSURANCE
Hymns Of Comfort
What A Friend What A Friend
Golden Bells
A Wonderful Savior A Wonderful Savior
Christ In Song Hymnal
Abide With Me Abide With Me
Christ In Song Hymnal
Glory Glory
Songs On Request