Khristu Mu Nyimbo

No description added.

Chichewa 220 Songs

Lowetsa Yesu Mu Mtima

[1]
Kodi watopa nazo zoipa, Lowetsa Yesu mu Mtima;
Ngati ufuna kutembenuka, Lowetsa Yesu mu Mtima.

Chorus;
Leka kukayikatu; Usamkanenso lero,
Tsegula Mtima wako; Lowetsa Yesu mu Mtima.

[2]
Ukafuna kukhala woyera, Lowetsa Yesu mu Mtima;
Madzi osamba ali pafupi, Lowetsa Yesu mu Mtima.

[3]
Ngati muli bvuto mtimamo, Lowetsa Yesu mu Mtima;
Ngati wapereweza za m’dziko, Lowetsa Yesu mu Mtima.

[4]
Abwenzi akakusandukira, Lowetsa Yesu mu Mtima;
Ndiye bwenzi losatekeseka, Lowetsa Yesu mu Mtima.

[5]
Ngati uyimba nao odala, Lowetsa Yesu mu Mtima;
Udzalowe m’nyumba za mpumulo, Lowetsa Yesu mu Mtima.

Chorus (wotsiriza)
Leka kukayikaku; Usamkanenso lero,
Ndatsegula citseko, Kuti Yesu alowemo.


Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffee Buy us a coffee

Like this song


Share this song

Lyrics Videos on Youtube

Holy, Holy, Holy Holy, Holy, Holy Hillsong United
AMAZING GRACE AMAZING GRACE Hymns Of Comfort
Ancient Words Ancient Words Golden Bells
Blessed Assurance Blessed Assurance Christ In Song Hymnal