Linda Usadandaule
[1]
Kwathu kosasinthikako, Ndi masautso kulibe;
Inde kwathu kowalako, Kodi sudzapumulako?
Chorus:
Linda, usadandauletu, Linda usadandauletu;
Linda, Linda, Usadandauletu.
[2]
Walemedwa ndi katundu, Wa zinthu za dziko lino,
Tsiku lopuma lidzadza( fatsa usadandaule.
[3]
M’njira muli minga kodi, Iye anabvala minga;
Wapeza cisoni kodi, Iye cinamgwera kale.
[4]
Gwira ntchito upirire, Ngakhale umanyozeka;
Tsiku lopuma lifika, Linda usadandaule.
Support Mysongbooks
Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.
Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.