Loading Songs...

Linda Ndi Kupemphera

[1]
Dikirani lero nthawi iri kutha;
Mungagwe m’zoipa linda ndi pemphero;
Thupi ndi lofoka mdaniyo ngwa mphamvu;
Dikirani nonse Mkwati ali kudza.

CHORUS;
Linda pempha, Linda pempha;
Usiku ndi usana dikirani ndi kupemphera.

(Tenor and Bass)
Linda pempha, linda pempha;
Linda pempha, linda pempha;
Usiku ndi usana dikirani ndi kupemphera.

[2]
Dzukani m’sagone musamakaika;
Mudzalandiratu mpumulo kumwamba;
Linda ndi pemphero, Mpulumutsi wanu,
Anasautsidwa cifukwa ca inu

[3]
Khulupira Yesu mdani ali pompo
Bvala zida zako mpaka Mbuye adze,
Musacedwe konse lero ndi labwino,
Dikirani nonse ndi kupempheranso.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

0 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

I WILL CALL UPON THE LORD I WILL CALL UPON THE LORD
Songs Of Prayer And Praise
HOLY HOLY HOLY HOLY HOLY HOLY
Songs Of Prayer And Praise
Wings Of A Dove Wings Of A Dove
Golden Bells
Holy, Holy, Holy Holy, Holy, Holy
Christ In Song Hymnal
Aliyeniokoa Aliyeniokoa
Kiswahili Praise And Worship