Loading Songs...

Ladzanso Tsiku Lakupumula

[1]
Ladzanso tsiku lakupula,
Lodalitsidwa ndi Mlunguyo;
Iye napuma ntchito zacezo,
Ndipo afuna tipumulenso.

[2]
Tiyeni tonse pa Sabatali,
Timveretu Kufuna kwaceko;
Tsono poyimba ndi kupemphera,
Iye adzakondwera nafetu.

[3]
Mbuye, Muchere khutu lanulo;
Mumve pemphero la t iana ’fe;
Kumbukirani lonjezanolo,
Mupulumutse otaikawo.

[4]
Inu, Atate wakumwambako,
Ndinu wakuticinjiriza ’fe.
Ndinu wakutitsogoleranso,
Tikuongani nthawi zonsezo.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

0 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

Umetamalaki Umetamalaki
Songs On Request
Hide Me, Rock Of Ages Hide Me, Rock Of Ages
Songs On Request
Mungu Mkuu Mungu Mkuu
Kiswahili Praise And Worship
10000 Reasons 10000 Reasons
Songs On Request
Aliyeniokoa Aliyeniokoa
Kiswahili Praise And Worship