Loading Songs...

Kwathu

[1]
Ndilakalaka kwathu! Dziko laufulu!
Kwathu kopanda mdima, Kulibe usiku;
Ndiri kulira kwathu, Mtima suli bwino;
Kulibe z owawa kwathu, Ndayandikirako;
Kulibe zowawa kwathu, Ndayandikirako.

[2]
Mbuyanga ali kwathu, Angelo abwino;
Kulibe chimo kwathu, Mayeso kulibe;
Nyimbozo za kwathuko Ndiri kuzimvatu
Ndikaganiza za kwathu Ndilira misozi
Ndikaganiza za kwathu Ndilira misozi

[3]
Anthu okhala kwathu Andikodolane,
Kopanda zacisoni Kwa okhala mommo;
Komomadi kwathuko! Kwa mtendere uko!
Kristu atifitsa kwathu Mwini wotikonda;
Kristu atifitsa kwathu Mwini wotikonda.


Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

0 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

Kaa Nami Kaa Nami
Kiswahili Praise And Worship
He Hideth My Soul He Hideth My Soul
Golden Bells
WHAT A FRIEND WE HAVE IN JESUS WHAT A FRIEND WE HAVE IN JESUS
Songs Of Prayer And Praise
Holy, Holy, Holy Holy, Holy, Holy
Hillsong United