Loading Songs...

Kunja Kuli Kuca Kodi

[1]
Kunja kuli kuca kodi? Mlonda, tandiuze ’ne.
Kodi nthanda yaturuka? Kodi kunja kwacatu?
Ukuona kodi kuti kwacadi?
Ukuona kodi kuti kwacadi?

[2]
Tifunsitse za ulendo, Kodi ulikuthadi?
Tayandikatu ku doko, Kodi tingaoneko?
Tingaone dziko lakumwambako?
Tingaone dziko lakumwambako?

[3]
Tipfuuletu kolimba, Kunja kuli kucatu;
Nthanda iri kuturuka, Ioneka mwambamo.
Kondwerani, tayandika kwathuko;
Kondwerani, tayandika kwathuko.

[4]
Tiri nao mau ace, Otitsogolera ’fe.
Tithamangetu dzolimba, Kuti tikafikeko.
Pfuulani mokondwera m’mtimamo
Pfuulani mokondwera m’mtimamo.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

0 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

Abide With Me Abide With Me
Christ In Song Hymnal
Does Jesus Care? Does Jesus Care?
Christ In Song Hymnal
ALL IN ALL ALL IN ALL
Songs Of Prayer And Praise