Kondi Dzina La Yesu
[1]
Konda dzinalo la Yesu, mwana wosauka ’we,
Ndilo lothandiza anthu, Khala nalo ponse phee.
Chorus:
Dzina la Yesuyo, Lokondwetsa onsewo.
Mwambamo, ponsepo, Litonthoza m’mtimamo.
[2]
Konda dzina la Yesu, M’moyo mwanu monsemo;
Mmene muli kuyesedwa, Chula dzina lacelo.
[3]
Dzina ili ndi lokoma, La Mombolo wathuyo,
Polandira ife mmwamba Tidzakondwererako.
[4]
Mbuye Yesu timtamanda, Ndi zinyimbo zathuzo;
Mfumu ya mafumu onse, Yesu timayesadi.
Support Mysongbooks
Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.
Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.