Kodi Ungakhale Moyo Wonga Wacewo
[1]
Kodi ungakhale moyo wacewo? Kumayenda naye m’njira monsemo?
Ungamlole Iye kunyamula nkhawazo? Mlole atsogole ’Ye.
Chorus:
Mwa mphamvu yace udzakhalatu, Wakumasuka, inde, m’wazi ’ce.
Cikondi ’ce cidzeze mtimako, Poyenda nawe zidamkonda ’Ye.
[2]
Ungamlole kuti Iye amasule ’we Kuti umutsate poitana ’Ye?
Ungamlole kucinjiriza Mbuyeyo? Mlole atsogole ’Ye.
[3]
Monga ukapeza malo mu ufumuwo? Ungamyese akusamalire ’we?
Ungagwire ntchito yace kopambanadi? Mlole atsogole ’Ye.
Support Mysongbooks
Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.
Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.