Loading Songs...

Kasupe Wa Madalitso

[1]
Idzani ndi madalitso, Mtima wanga uyimbe;
Nsisi zanu zisaleke, Kuti tiyamike ’Nu
Phunzitsani kumvera ’Nu, kuti ndikudziweni,
Pamene ciyembekezo Cidzaza Mtima wanga.

[2]
Ndinutu thandizo langa, Mwandifikitsa pano,
Ndipo mwa cifundo canu Ndikafika kwathuko.
Anandifuna Yesuyo, Posocera mtarimo;
Anakhetsa mwazi wace kundiombola ine.

[3]
M’ndipatse cisomo canu, Pakuti ndicisowa
Mundikokere kwa Inu Ndi cikondi canuno.
Sindifuna kusocera, Kukusiyani Inu
Tengani Mtima wangawu; Ukhale wanu konse


Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

2 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

Does Jesus Care? Does Jesus Care?
Spiritual Songs
Joy To The World Joy To The World
Caroling Songs
GIVE THANKS GIVE THANKS
Songs Of Prayer And Praise
Amazing Grace Amazing Grace
Spiritual Songs