Loading Songs...

Kapenatu Si Ku Phriko

[1]
Kapenatu si ku phiriko, Kapena ku nyanjako,
Kapena ku nkhondo komwetu, Mufuna ndipite ’ne;
Komatu akandituma ’ne Ku dziko la ’lendowo,
Ndilola mwa mphamvu ya Mbuyeyo, Ndzapita mufunako.

Chorus:
Ndzapita kulmene mufunako, M’phiri, m’dambo, ndi m’nyanja
Ndzanena zimene mufunazo, Ndzatsata Mpulumutsiyo

[2]
Alipo mau Ambuyeyo, Afuna ndinetu;
Kapena kuli wocimwayo Wosowa thandizoli;
Ambuye, mkanditsogoza ’ne, Ingabvute njirayo,
Ndzauza uthenga wabwinowo, Ndzanena mufunazo.

[3]
Alipo malo a inenso Ku munda wa Mbuyeyo,
Ndzagwira ntchito yotutayo Ya Yesu wopacikwa.
Pokhulupirira mwanumo, podziwa mndikonda ’ne,
Ndzacita kufunatu kwanuko, Ndzakhala mufunazo.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

0 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

Amazing Grace Amazing Grace
Golden Bells
Glory Glory
Songs On Request
Joy To The World Joy To The World
Caroling Songs
Amazing Grace Amazing Grace
Spiritual Songs
Blessed Assurance Blessed Assurance
Spiritual Songs