Khristu Mu Nyimbo

No description added.

Chichewa 220 Songs

Inetu Ndifunadi

[1]
Inetu ndifunadi Kufanana ndi Yesu,
Andidzaze mtimamo Ndi kufatsa kwaceko;
Ndidziyenda monga ’Ye mdziko la zoipali;
Ndine wosaukadi, Yesu mkhale mtimanga.

[2]
Ngati amva kwangwala, Nayang’ana mphetazo,
Nasamala zonsezo, Ndithu andimveranso
Adzandiphunzitsa ’ne, Nakhulukira ’ne;
Ndikhaletu wagwiro, Yesu mkhale mtimanga.

[3]
Popemphera ndikhale Monga Yesu Mbuyeyo;
Ndipumule mwa Iye, Andimwetse madziwo.


Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffee Buy us a coffee

Like this song


Share this song

Lyrics Videos on Youtube

Holy, Holy, Holy Holy, Holy, Holy Hillsong United
AMAZING GRACE AMAZING GRACE Hymns Of Comfort
Ancient Words Ancient Words Golden Bells
Blessed Assurance Blessed Assurance Christ In Song Hymnal