Loading Songs...

Idzani Nonsenu Okonda Yesu

[1]
Idzani nonsenu, Okonda Yesuyo,
Tiyimbe nyimbo yabwino, Tiyimbe nyimbo yabwino
Ku mpando wacewo, Ku mpando wacewo.

CHORUS:
Tiyende (tu) pamodzi, Tirikupita kumwamba;
Akristu tirikupita (pita), ku Zioni wabwainoyo.

[2]
Ngkhale enawo Aleke kwimbako,
Akristu ’fe tidzayimba, Akristu ’fe tidzayimba
Kumlemekeza ’ye, kumlemekezaye

[3]
Akristu tonsefe, Tikondwe mdzikoli
Koposa anthu enawo, Koposa anthu enawo,
Tisanafikeko, Tisanafikeko.

[4]
Tiyimbe mokondwa, Misozi iume;
Poyenda kunka kwathuko, Poyenda kunka kwathuko,
Kwa Mlungu wathuyo, Kwa Mlungu wathuyo.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

0 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

BLESSED ASSURANCE BLESSED ASSURANCE
Songs Of Prayer And Praise
AMAZING GRACE AMAZING GRACE
Hymns Of Comfort
Joy To The World Joy To The World
Christ In Song Hymnal
ALL IN ALL ALL IN ALL
Songs Of Prayer And Praise