Loading Songs...

DzuWa Liri Kulowa

[1]
Dzuwa liri kulowa, Mlungu atipumitse;
Linda ndi kupemphera mmene nyali ziri kuwala m’mwamba.

CHORUS:
Woyera Ambuye wa makamu!
Za m’mwamba ndi za dziko zitamanda Inu
Mlungu Wamkuru.

[2]
Ambuye wamoyo’Nu, Ife tasonkhanatu
Kufuna nkhope Yanu; mutifungatire’fe m’khola Lanu

[3]
Pamene mthunzi ugwa, Mumatifungatira;
Mwa cisomo canutu, Mitima yathu ikwera kwa Inu.

[4]
Tikamwalira ife osaona za dziko,
Ambuye wacifundo, mutidzutsenzo tsiku lotsiriza.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

0 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

Umetamalaki Umetamalaki
Songs On Request
Immortally Arrayed Immortally Arrayed
Songs On Request
Joy to the World Joy to the World
Sunday School Songs
Kutembea Nawe Kutembea Nawe
Kiswahili Praise And Worship