Loading Songs...

Dzina Lopambana Mmwamba

[1]
Dzina lopambana m’mwamba, Ndi pa dzilo lonselo,
Lomwe ’Tate anamucha Mwana wace mmodziyo.

CHORUS:
Dzina loyeratu (loyera), Dzina lofatsanso (lofatsa),
Lomwe nalinena angelowo.
Pa utsiku uja (dzinalo), Dzina lokomatu (dzinalo),
Ndilo la Ambuye Yesu.

[2]
Dzinalo lipatsa dalo, Ndi cimwemwe mtimanga,
Ndidzauza anthu ena Za cokoma caceco.

[3]
Moyo wanga udzayimba Za cikondi caceco;
Ndidzatamandabe dzina, Lopambana onsewo.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

1 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

Moyo Wangu Sifu Bwana Moyo Wangu Sifu Bwana
Kiswahili Praise And Worship
Kaa Nami Kaa Nami
Kiswahili Praise And Worship
Wade In The Water Wade In The Water
Songs On Request
JOY TO THE WORLD JOY TO THE WORLD
Songs Of Prayer And Praise
Aliyeniokoa Aliyeniokoa
Kiswahili Praise And Worship