Loading Songs...

Cinthu Cina Kwa Yesu

[1]
Mbuye! Cikondico ’natifera,
Cosandiyenera, ndidza kwanu;
Ndidziperekatu mphatso zanga zonse,
Sindidzamanatu cirri conse.

[2]
Wondipembedzera ndinu nokha
Ndiyembekezera pa Inutu;
Senzeni mtandawo ndiuze cikondi
Kuti ndingacite cinthu cina.

[3]
Zonse ndiri nazo nzolandira
Monga masikuwa’ kupita,
Ntchito yacikondi yayambidwa kale,
Otaika ena tikabweze.

[4]
Zonse ndiri nazo mwandipatsa,
Ndipatsa kwa Inu Ambuyanga
Nditafika m’mwamba moyo wanga ngwanu,
Cinthu cina nchanu nthawi zonse.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

3 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

Joy to the World Joy to the World
Sunday School Songs
ALL IN ALL ALL IN ALL
Songs Of Prayer And Praise
JOY TO THE WORLD JOY TO THE WORLD
Songs Of Prayer And Praise
He Hideth My Soul He Hideth My Soul
Golden Bells
He Gave Me A Song He Gave Me A Song
Songs On Request
Does Jesus Care? Does Jesus Care?
Spiritual Songs