Loading Songs...

Cimwemwe Posacedwa

[1]
Cimwemwe podzatha ntchitoyi, Podzasonkhana okukha,
Alikudza ndi zipatso, Ku Yerusalemuko.

CHORUS:
Kudzakhala cimwemwedi,
Cimwemwe ca nthawi zonse,
Cifukwa nthawi yafika,
Yosankhana okunkha.

Bass ndi Tenor:
Cimwemwe posacedwa,
Cimwemwe ca muyaya,
Chifukwa nthawi yafika,
Yosonkhana okunkha.

[2]
Tidzayimba nyimbo zabwino, Tidzayamika mokondwa,
Tidzatama Kristu Mfumu, Mu mzinda watsopano.

[3]
Cimwemwe citidikirako, Ku malo a cikhuduwo;
Yesu ali kuwakonza, Mu Mzinda watsopano.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

1 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

Come We That Love The Lord Come We That Love The Lord
Christ In Song Hymnal
HE HIDETH MY SOUL HE HIDETH MY SOUL
Hymns Of Comfort
BLESSED ASSURANCE BLESSED ASSURANCE
Songs Of Prayer And Praise
Joy To The World Joy To The World
Christ In Song Hymnal
HOW GREAT THOU ART HOW GREAT THOU ART
Songs Of Prayer And Praise