Loading Songs...

Cidzakhala Cimwemwe

[1]
Cidzakhala cimwemwe coposa,
potsamira m’mikono mwace;
Kuli dalo kwa Mlungu wangayo,
potsamira m’mikono mwace.

CHORUS:
Potsamira, Adzandipulumutsatu;
Mwa zoopsya, Potsamira m’mikono mwace.

Bass and tenor:

Potsamiratu, Potsamiratu, Adzandipulumutsatu;
Mwa zoopsyazo, Mwa zoopysazo,
Potsamira m’mikono mwace.

[2]
Nkwambinotu kuyenda m’njirayi,
Potsamira m’mikono mwace;
Njowaladi koposa njirayi,
Potsamira m’mikono mwace.

[3]
Ndiopanji ndi kuda nkhawanso,
Potsamira m’mikono mwace?
mbuyanga ali nane pafupi,
Potsamira m’mikono mwace.




Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

1 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

Victory In Jesus Victory In Jesus
Golden Bells
Here I Am To Worship Here I Am To Worship
Hillsong United
Servant’s Song Servant’s Song
Songs On Request
I LOVE YOU LORD I LOVE YOU LORD
Songs Of Prayer And Praise