Loading Songs...

Anandibvuula

[1]
Mtima wanga unaopa Yehova
Ntakanikizidwa pansi ndi cimo;
Ndamulirira Ambye m’thopemo,
Anandibvuulamo mwa cifundo.

Chorus:
Anandibuula m’matope,
Nandikhazikitsa pa thanthwe;
Moyo wanga lero uyimba,
Matamando Haleluya

[2]
Wandikhazika pa thanthwe lolimba,
Ndakhazikitsidwa sindicokapo;
Pano palibe coopsya ndakhala,
Cisomo cidzandibveka korona.

[3]
Wandipatsa nyimbo ya mayamiko,
Msana ndi usiku ndidzayimba;
Mtimawu useka ndi ufulu,
Ndikutamandani Mombolo wanga.

[4]
Ndidzayimba nsisi mwandicitira,
Ndzalimbika mpaka onse amdziwe;
Cipulumutso ndzayimba konseko.
Kuti ambiri amvere Mulungu.


Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

1 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

HOLY HOLY HOLY HOLY HOLY HOLY
Songs Of Prayer And Praise
Jesus My Savior Jesus My Savior
Songs On Request
Joy To The World Joy To The World
Caroling Songs
Amazing Grace Amazing Grace
Spiritual Songs
JOY TO THE WORLD JOY TO THE WORLD
Songs Of Prayer And Praise