Loading Songs...

Ambuye Wathu Yesu, Mubwera Liti

[1]
Ambuye wathu Yesu, Mubwera liti ko?
Mitima yatopadi, Mucedweranji ko?
Lidzadza liti tsiku lonyezimiralo
Limene anthu anu adzakondweranso?

[2]
Musiya mpaka liti, Ee, nyumba yanuyo?
Mwacedwacedwa, Mbuye, Ambiri agwatu;
Agwidwa ndi za dziko, Antchito anuwo;
Atsalatu pang’ono Oyang’anira ’Nu.

[3]
Dzutsani anthu anu, Tumani mauwo;
Amene anthu onse, Akudza Mbuyeyo!
Ziyake nyali zathu, tibvale bwinotu
Tikonze Mtima wathu, Kuona Mbuyeyo.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

3 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

Kutembea Nawe Kutembea Nawe
Kiswahili Praise And Worship
MARCHING TO ZION MARCHING TO ZION
Songs Of Prayer And Praise
Wings Of A Dove Wings Of A Dove
Golden Bells
GREAT IS THY FAITHFULNESS GREAT IS THY FAITHFULNESS
Hymns Of Comfort