Loading Songs...

Ambuyanga Yesu, Ndikonda Inu

[1]
Ambuyanga Yesu, Ndikonda Inu,
Ndisiya zoipa cifukwa canu;
Ambuye wabwino ndi Mplumutsiyo;
Ndikonda tsopano koposa kale.

[2]
Ndikonda cifukwa munakonda ’ne;
Mnafera pa mtengo kuombola ’ne;
Mukhululukira zoipa zones;
Ndikonda tsopano koposa kale.

[3]
Ndizakukondani kosalekai,
Ndidzakututamani masiku onse.
Mpakatu ndidzafa ndidzanenabe,
Ndikonda tsopano koposa kale.

[4]
Ku malo owalo kumwamba komwe
Ndidzakuongani, Ambuye Yesu;
Ntabvala korona ndizayimbabe,
Ndkonda tsopano koposa kale.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

4 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

Kutembea Nawe Kutembea Nawe
Kiswahili Praise And Worship
God Bless You, Go With God God Bless You, Go With God
Songs On Request
AMAZING GRACE AMAZING GRACE
Hymns Of Comfort
Abide With Me Abide With Me
Golden Bells