Loading Songs...

Ali Kudza

[1]
Timamva uthenga wabwinotu, M’mene tiri kunka kwathu
Msanga Mpulumutsi adzabwera, kukhala mfumu yathu

Chorus:
Ali kudza posacedwa, Inde ali kudza pa dzikoli
Ndipo tidzapita tonse kumwamba, Pakubwera Yesuyo.

[2]
Manda a anthu oyera mtima, Adzatsegulidwa ndithu
Ndipo onse ogonera m’mandamo, Adzakhalanso moyo.

[3]
Sitidzalekananso kwathu ko, Tidzayimba za chombolo;
Anthu a mitundu yonse adzadza, kupembedza Mfumuyo.

[4]
Tidzayimba aleluya, Amen! Msanga tikasamalira;
Dikirani ndi kupemphera nonse Tidzabvala korona.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

3 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

Hide Me, Rock Of Ages Hide Me, Rock Of Ages
Songs On Request
What A Friend What A Friend
Golden Bells
Servant’s Song Servant’s Song
Songs On Request
When The Roll Is Called Up Yonder When The Roll Is Called Up Yonder
Christ In Song Hymnal