Loading Songs...

Akristu Limbikani!

[1]
Akristu limbikani, imani mtimanji!
Mbendera nyamulani, musanthenthemerebi.
Wotsogolera wathu ndi Mwana wa Mulungu;
Adzagonjetsa onse, adani athuwo.

[2]
Tigwire nkhondo yomwe ya Mbuye wathuyo;
Ticotse zakuipa zokhala mtimamo.
Sitikwanira tokha kuleka zinthu zomwe;
Koma Mbuyathu Yesu atithangatatu.

[3]
Tsopano timenyana ndi zakuipazo,
Pamene nkhondo yatha tidzanka kwathuko;
Yesu adzalandira ankhondo ace onse,
Adzakhalitsa naye Kumwamba komweko.

[4]
Limbikani anzathu! Msanga nkhondo itha
Lero kuli cinkhondo, mawa tigonjetsa
Kwa iye wolakika, adzakhala moyo;
Pamodzi ndi Mfumuyo ’dzakhala kosatha.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

12 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

Wings Of A Dove Wings Of A Dove
Golden Bells
I LOVE YOU LORD I LOVE YOU LORD
Songs Of Prayer And Praise
Come Unto Me Come Unto Me
Christ In Song Hymnal
Jesus My Savior Jesus My Savior
Songs On Request
Kutembea Nawe Kutembea Nawe
Kiswahili Praise And Worship
I'LL FLY AWAY I'LL FLY AWAY
Songs Of Prayer And Praise