Loading Songs...

Akristu Ali Naco Ciyembekezo

[1]
Akristu ali nacotu Ciyembekezoco
Cimatikondweretsatu M’mabuto monsemo
Cimatikondweretsatu M’mabuto monsemo.

[2]
Cinema za mpumulowo Pokhala ndi Kristu.
Pamodzi ndi anzangawo tidzakhalitsako.
Pamodzi ndi anzangawo Tidzakhalitsako.

[3]
Mayeso ndi macimowo Kulibe mdzikolo.
Misozi ndipo imfanso kulibe komweko
Misozi ndipo imfanso kulibe komweko.

[4]
Masiku athe msangatu, Ambuye Adzetu.
Tilakalaka kuona Dzikolo ndi Inu
Tilakalaka kuona Dzikolo ndi Inu



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

3 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

Mungu Mkuu Mungu Mkuu
Kiswahili Praise And Worship
Does Jesus Care? Does Jesus Care?
Christ In Song Hymnal
How Great Thou Art How Great Thou Art
Spiritual Songs
GIVE THANKS GIVE THANKS
Songs Of Prayer And Praise
Joy To The World Joy To The World
Christ In Song Hymnal