Loading Songs...

’Mvani Yesu Aitana

[1]
’Mvani Yesu aitana, Ndani angagwiretu?
Mindayo yayera kale, Ndani akakunkhemo?
Momvekadi aitana, Mphotho ’dzalandira ’we
Ndani angayankhe msanga, Ndine Mbuye, tumeni.

[2]
Nkana sungapite mtari Ku maiko enawo,
Ungapeze anthu ena Apafupi ndi iwe.
Ngati sungalalikire mnga ngati Paulo,
Unganene za cikondi Ca Ambuye wakoyo.

[3]
Ngati sungakhale mlonga Wocenjeza anthuwo;
Kuwauza anthu njira yonka nayo mmwambamo;
Pakupempherera ena, Ungagwire ntchitoyo.
Ungacite ngati Huri pothangata Moseyo.

[4]
Mmene anthu alikufa, Mbuye aitanabe;
Wina asamamve nuti, singacite kanthui.
Gwira antchito wakupatsa, Nuigwire msangatu;
Ndi kuyankha poitana, Ndine Mbuye, tumeni.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

3 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

He Gave Me A Song He Gave Me A Song
Songs On Request
See, What A Morning See, What A Morning
Songs On Request
ABIDE WITH ME ABIDE WITH ME
Hymns Of Comfort
HOW GREAT THOU ART HOW GREAT THOU ART
Songs Of Prayer And Praise
Joy to the World Joy to the World
Sunday School Songs