Loading Songs...

Khalatu Woyera

[1]
Khalatu woyera, Pemphera mtseri;
Werenga mau ’ce, Masiku once;
Thangatani omwe Ali ofo’oka,
Madalitso ace Funanani.

[2]
Khalatu woyera, Dziko laipa;
Pemphera kolimba, Kwa Yesu Mbuye;
Yang’anitsa Yesu, Ndi Kumtsatira
Kuti anthu ena, Aone Yesu.

[3]
Khalatu woyera, Akutsogoze,
Usamtsogolere, m’njira zakozo;
M’nsoni ndi pokondwa, Tsata Mbuyako
Khulupira Yesu Ndi mau ace.

[4]
Khalatu woyera, Khala wofatsa,
Alamulire ’Ye, Ganizo lako;
Utatsogozedwa Ndi Mzimu wace,
Msanga udzagwira Ntchito ya mmwamba.



Support Mysongbooks

Support us by joining the Buy Me A Coffee community and making a small donation, you can help us expand our library and ensure that music lovers everywhere can enjoy their favorite songs to the fullest. We're passionate about music, and we know you are too, so let's work together to keep the music alive.

Thank you for being a part of our community and supporting our mission to provide the best lyrics library on the internet.

Buy me a coffeeBuy us a coffee

Like this song

1 Likes

Share this song

Facebook WhatsApp Twitter Telegram LinkedIn Email

Lyrics Videos on Youtube

Abide With Me Abide With Me
Golden Bells
Kutembea Nawe Kutembea Nawe
Kiswahili Praise And Worship
Ill Fly Away Ill Fly Away
Golden Bells
DOES JESUS CARE? DOES JESUS CARE?
Hymns Of Comfort
Wings Of A Dove Wings Of A Dove
Golden Bells
Mungu Mkuu Mungu Mkuu
Kiswahili Praise And Worship